Lyrics
🎙️ V3nja – ZANGA (Lyrics)
Tich Da!
It’s Boy V3NJA!
[Verse 1]
Koma lija n'kale
Munatemga ndalama zanga
Inu Mr. Mwale
Kapena munkafuna ndiiwale
Mwachulusa mabodza
Inu ndi tambawali eti?
Koma zanga ndizifuna
[Pre-Chorus]
Paja umangoti mawa, mawa, mawa
Koma mawa silifika
Koma mawa silifika
Paja umangoti mawa, mawa, mawa
Koma mawa silifika
Koma mawa silifika
[Chorus]
Ndikufuna zanga
Mundibwenzere zanga
Ndikufuna zanga
Mundibwenzere zanga
Muli ndi zanga
Mundibwenzere zanga
Ndikufuna zanga
Mundibwenzere zanga
(Aa aa aa aaah)
[Post-Chorus]
Mundibwenzere, mundibwenzere
Eeh mundibwenzere
Mundibwenzere, mundibwenzere
Eeh mundibwenzere
Mundibwenzere, mundibwenzere
Eeh mundibwenzere
Mundibwenzere, mundibwenzere
Eeh mundibwenzere
[Verse 2]
Mesa unkati wavutika
Ine pokumvera chisoni ndinakutandiza
Zabwino waiwala
Wayamba kundiponya miyala
Ukulenga misala
Wayambapo kuluma no chala
Chinakudyesa phala
[Pre-Chorus – Repeat]
Paja umangoti mawa, mawa, mawa
Koma mawa silifika
Koma mawa silifika
Paja umangoti mawa, mawa, mawa
Koma mawa silifika
Koma mawa silifika
[Chorus – Repeat]
Ndikufuna zanga
Mundibwenzere zanga
Ndikufuna zanga
Mundibwenzere zanga
Muli ndi zanga
Mundibwenzere zanga
Ndikufuna zanga
Mundibwenzere zanga
(Aa aa aa aaah)
[Post-Chorus – Repeat]
Mundibwenzere, mundibwenzere
Eeh mundibwenzere
Mundibwenzere, mundibwenzere
Eeh mundibwenzere
Mundibwenzere, mundibwenzere
Eeh mundibwenzere
Mundibwenzere, mundibwenzere
Eeh mundibwenzere